Luka 3:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pamene anthu onse anali kubatizidwa, Yesu+ nayenso anabatizidwa. Ndipo pamene anali kupemphera, kumwamba+ kunatseguka.
21 Pamene anthu onse anali kubatizidwa, Yesu+ nayenso anabatizidwa. Ndipo pamene anali kupemphera, kumwamba+ kunatseguka.