Luka 11:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 “Tsoka inu odziwa Chilamulo, chifukwa munalanda anthu kiyi yowathandiza kudziwa zinthu.+ Inuyo simunalowemo, ndipo ofuna kulowamo munawatsekereza!”+
52 “Tsoka inu odziwa Chilamulo, chifukwa munalanda anthu kiyi yowathandiza kudziwa zinthu.+ Inuyo simunalowemo, ndipo ofuna kulowamo munawatsekereza!”+