Machitidwe 20:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndikudziwa kuti ine ndikachoka, mimbulu+ yopondereza idzafika pakati panu ndipo sidzasamalira gulu la nkhosa mwachikondi. 1 Timoteyo 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Komabe, mawu ouziridwa amanenadi kuti m’nthawi zam’tsogolo,+ ena adzagwa+ pa chikhulupiriro, chifukwa chomvetsera mawu ouziridwa omwe ndi osocheretsa,+ ndiponso ziphunzitso za ziwanda.+
29 Ndikudziwa kuti ine ndikachoka, mimbulu+ yopondereza idzafika pakati panu ndipo sidzasamalira gulu la nkhosa mwachikondi.
4 Komabe, mawu ouziridwa amanenadi kuti m’nthawi zam’tsogolo,+ ena adzagwa+ pa chikhulupiriro, chifukwa chomvetsera mawu ouziridwa omwe ndi osocheretsa,+ ndiponso ziphunzitso za ziwanda.+