Mateyu 24:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 chifukwa ambiri adzabwera m’dzina langa ndi kunena kuti, ‘Khristu uja ndine,’ ndipo adzasocheretsa anthu ambiri.+ Luka 17:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndipo anthu adzakuuzani kuti, ‘Onani uko!’ kapena ‘Onani kuno!’+ Musadzapiteko kapena kuwatsatira.+
5 chifukwa ambiri adzabwera m’dzina langa ndi kunena kuti, ‘Khristu uja ndine,’ ndipo adzasocheretsa anthu ambiri.+
23 Ndipo anthu adzakuuzani kuti, ‘Onani uko!’ kapena ‘Onani kuno!’+ Musadzapiteko kapena kuwatsatira.+