Luka 17:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Choncho iwo anamufunsa kuti: “Kodi zimenezi zidzachitikira kuti Ambuye?” Iye anawauza kuti: “Kumene kuli thupi lakufa,+ ziwombankhanga zidzasonkhana komweko.”+
37 Choncho iwo anamufunsa kuti: “Kodi zimenezi zidzachitikira kuti Ambuye?” Iye anawauza kuti: “Kumene kuli thupi lakufa,+ ziwombankhanga zidzasonkhana komweko.”+