Aheberi 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Zimenezi zidzatha, koma inu mudzakhalapo mpaka muyaya. Ndipo zonsezi zidzatha ngati mmene malaya akunja amathera.+
11 Zimenezi zidzatha, koma inu mudzakhalapo mpaka muyaya. Ndipo zonsezi zidzatha ngati mmene malaya akunja amathera.+