Mateyu 25:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mbuye wakeyo anamuyankha kuti, ‘Wachita bwino kwambiri, kapolo wabwino ndi wokhulupirika iwe!+ Unakhulupirika+ pa zinthu zochepa. Ndikuika kuti udziyang’anira zinthu zambiri.+ Sangalala+ limodzi ndi ine mbuye wako.’ Luka 12:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Ndithu ndikukuuzani, Adzamuika kukhala woyang’anira zinthu zake zonse.+
21 Mbuye wakeyo anamuyankha kuti, ‘Wachita bwino kwambiri, kapolo wabwino ndi wokhulupirika iwe!+ Unakhulupirika+ pa zinthu zochepa. Ndikuika kuti udziyang’anira zinthu zambiri.+ Sangalala+ limodzi ndi ine mbuye wako.’