Luka 19:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho iye ananena kuti: “Munthu wina wa m’banja lachifumu anapita kudziko lakutali kuti akalandire ufumu ndi kubwerako.+
12 Choncho iye ananena kuti: “Munthu wina wa m’banja lachifumu anapita kudziko lakutali kuti akalandire ufumu ndi kubwerako.+