Mateyu 18:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “N’chifukwa chake ufumu wakumwamba uli ngati mfumu+ imene inafuna kuti akapolo ake abweze ngongole.+ Luka 19:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Atabwerera kwawo pambuyo polandira ufumuwo, analamula kuti akapolo ake aja amene anawapatsa ndalama zasiliva abwere kwa iye, kuti awerengerane ndi kuona mmene apindulira pa malonda awo.+
23 “N’chifukwa chake ufumu wakumwamba uli ngati mfumu+ imene inafuna kuti akapolo ake abweze ngongole.+
15 “Atabwerera kwawo pambuyo polandira ufumuwo, analamula kuti akapolo ake aja amene anawapatsa ndalama zasiliva abwere kwa iye, kuti awerengerane ndi kuona mmene apindulira pa malonda awo.+