Mateyu 21:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kenako iye anawasiya n’kutuluka mumzindawo kupita ku Betaniya, ndipo anagona kumeneko.+