Yohane 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma iye ponena izi sikuti anali kudera nkhawa osauka ayi, koma chifukwa anali wakuba.+ Iye anali wosunga bokosi la ndalama,+ ndipo anali kutengamo ndalama zimene zinali kuponyedwa m’bokosilo.
6 Koma iye ponena izi sikuti anali kudera nkhawa osauka ayi, koma chifukwa anali wakuba.+ Iye anali wosunga bokosi la ndalama,+ ndipo anali kutengamo ndalama zimene zinali kuponyedwa m’bokosilo.