Maliko 14:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma Yesu anati: “Mulekeni. N’chifukwa chiyani mukum’vutitsa mayiyu? Iyetu wandichitira zinthu zabwino.+
6 Koma Yesu anati: “Mulekeni. N’chifukwa chiyani mukum’vutitsa mayiyu? Iyetu wandichitira zinthu zabwino.+