Maliko 14:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mayiyu wachita zimene angathe. Iye wapakiratu thupi langa mafuta onunkhira kukonzekera kuikidwa kwanga m’manda.+ Yohane 12:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho Yesu anati: “M’lekeni, achite mwambo umenewu pokonzekera tsiku limene ndidzaikidwe m’manda.+
8 Mayiyu wachita zimene angathe. Iye wapakiratu thupi langa mafuta onunkhira kukonzekera kuikidwa kwanga m’manda.+
7 Choncho Yesu anati: “M’lekeni, achite mwambo umenewu pokonzekera tsiku limene ndidzaikidwe m’manda.+