1 Akorinto 11:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Anachitanso chimodzimodzi ndi kapu+ atadya chakudya chamadzulo, ndipo anati: “Kapu iyi ikutanthauza pangano latsopano+ pamaziko a magazi anga.+ Muzichita zimenezi nthawi zonse pamene mukumwa za m’kapu imeneyi pondikumbukira.”+
25 Anachitanso chimodzimodzi ndi kapu+ atadya chakudya chamadzulo, ndipo anati: “Kapu iyi ikutanthauza pangano latsopano+ pamaziko a magazi anga.+ Muzichita zimenezi nthawi zonse pamene mukumwa za m’kapu imeneyi pondikumbukira.”+