Yeremiya 31:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 “Taonani! Masiku adzafika, pamene ndidzachita pangano latsopano+ ndi nyumba ya Isiraeli+ komanso ndi nyumba ya Yuda,”+ watero Yehova. Aheberi 7:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pa chifukwa chimenecho, Yesu wakhala chikole cha pangano labwino koposa.+ Aheberi 9:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Iye anati: “Awa ndi magazi a pangano limene Mulungu wakulamulani kuti mulisunge.”+
31 “Taonani! Masiku adzafika, pamene ndidzachita pangano latsopano+ ndi nyumba ya Isiraeli+ komanso ndi nyumba ya Yuda,”+ watero Yehova.