Maliko 14:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Nthawi yomweyo, mawu adakali m’kamwa, Yudasi, mmodzi wa ophunzira ake 12 aja, anafika limodzi ndi khamu la anthu kuchokera kwa ansembe aakulu ndi alembi ndi akulu, atanyamula malupanga ndi zibonga.+
43 Nthawi yomweyo, mawu adakali m’kamwa, Yudasi, mmodzi wa ophunzira ake 12 aja, anafika limodzi ndi khamu la anthu kuchokera kwa ansembe aakulu ndi alembi ndi akulu, atanyamula malupanga ndi zibonga.+