Luka 4:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Choncho anapita ku Kaperenao,+ mzinda wa ku Galileya. Ndipo anali kuwaphunzitsa pa sabata. Yohane 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Izi zitatha, iye, mayi ake, abale ake+ ndi ophunzira ake anapita ku Kaperenao,+ koma kumeneko sanakhaleko masiku ambiri.
12 Izi zitatha, iye, mayi ake, abale ake+ ndi ophunzira ake anapita ku Kaperenao,+ koma kumeneko sanakhaleko masiku ambiri.