Maliko 14:53 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 53 Tsopano iwo anatengera Yesu kwa mkulu wa ansembe, ndipo ansembe aakulu komanso akulu ndi alembi onse anasonkhana kumeneko.+ Yohane 18:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choyamba anapita naye kwa Anasi, pakuti anali mpongozi wa Kayafa, amene anali mkulu wa ansembe chaka chimenecho.+
53 Tsopano iwo anatengera Yesu kwa mkulu wa ansembe, ndipo ansembe aakulu komanso akulu ndi alembi onse anasonkhana kumeneko.+
13 Choyamba anapita naye kwa Anasi, pakuti anali mpongozi wa Kayafa, amene anali mkulu wa ansembe chaka chimenecho.+