Maliko 14:62 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 62 Pamenepo Yesu anati: “Inde ndinedi, ndipo anthu inu mudzaona Mwana wa munthu+ atakhala kudzanja lamanja+ lamphamvu. Mudzamuonanso akubwera ndi mitambo yakumwamba.”+
62 Pamenepo Yesu anati: “Inde ndinedi, ndipo anthu inu mudzaona Mwana wa munthu+ atakhala kudzanja lamanja+ lamphamvu. Mudzamuonanso akubwera ndi mitambo yakumwamba.”+