Maliko 14:67 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 67 Ataona Petulo akuwotha moto, anamuyang’anitsitsa ndi kunena kuti: “Inunso munali ndi Yesu, Mnazareti uja.”+ Yohane 18:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Pa nthawiyi Simoni Petulo anali ataimirira akuwotha moto. Pamenepo iwo anamufunsa kuti: “Kodi iwenso si iwe mmodzi wa ophunzira ake?” Iye anakana n’kunena kuti: “Ayi si ine.”+
67 Ataona Petulo akuwotha moto, anamuyang’anitsitsa ndi kunena kuti: “Inunso munali ndi Yesu, Mnazareti uja.”+
25 Pa nthawiyi Simoni Petulo anali ataimirira akuwotha moto. Pamenepo iwo anamufunsa kuti: “Kodi iwenso si iwe mmodzi wa ophunzira ake?” Iye anakana n’kunena kuti: “Ayi si ine.”+