Yesaya 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Anthu amene anali kuyenda mu mdima, aona kuwala kwakukulu.+ Anthu amene anali kukhala m’dziko la mdima wandiweyani,+ kuwala kwawawalira.+
2 Anthu amene anali kuyenda mu mdima, aona kuwala kwakukulu.+ Anthu amene anali kukhala m’dziko la mdima wandiweyani,+ kuwala kwawawalira.+