Maliko 15:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pamenepo iwo anafuula kuti: “M’pachikeni!”+ Luka 23:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pamenepo anthuwo anayamba kufuula kuti: “M’pachikeni! M’pachikeni!”+