Deuteronomo 21:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno akulu onse a mzinda umene uli pafupi ndi munthu wophedwayo azisamba m’manja+ pamwamba pa ng’ombe imene yathyoledwa khosi m’chigwa ija.
6 Ndiyeno akulu onse a mzinda umene uli pafupi ndi munthu wophedwayo azisamba m’manja+ pamwamba pa ng’ombe imene yathyoledwa khosi m’chigwa ija.