Yohane 1:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Kenako iye anapita naye kwa Yesu. Yesu atamuyang’ana+ anati: “Iwe ndiwe Simoni+ mwana wa Yohane,+ udzatchedwa Kefa” (dzina limene kumasulira kwake ndi Petulo).+
42 Kenako iye anapita naye kwa Yesu. Yesu atamuyang’ana+ anati: “Iwe ndiwe Simoni+ mwana wa Yohane,+ udzatchedwa Kefa” (dzina limene kumasulira kwake ndi Petulo).+