Luka 23:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Komanso onse amene anali kumudziwa anaimirira chapatali ndithu.+ Ndipo amayi amene anamutsatira kuchokera ku Galileya, anaimiriranso chapomwepo n’kumaonerera zinthu zimenezi.+
49 Komanso onse amene anali kumudziwa anaimirira chapatali ndithu.+ Ndipo amayi amene anamutsatira kuchokera ku Galileya, anaimiriranso chapomwepo n’kumaonerera zinthu zimenezi.+