Mateyu 28:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 n’kuwauza kuti: “Muzinena kuti, ‘Ophunzira ake+ anabwera usiku kudzamuba ife titagona.’