Danieli 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiyeno anabweretsa mwala ndi kutseka pakhomo la dzenjelo. Kenako mfumu inadinda mwalawo ndi mphete yake yodindira ndipo nduna zakenso zinaudinda ndi mphete yawo yodindira, kuti chilichonse chokhudza Danieli chisasinthidwe.+
17 Ndiyeno anabweretsa mwala ndi kutseka pakhomo la dzenjelo. Kenako mfumu inadinda mwalawo ndi mphete yake yodindira ndipo nduna zakenso zinaudinda ndi mphete yawo yodindira, kuti chilichonse chokhudza Danieli chisasinthidwe.+