Maliko 16:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma atayang’anitsitsa, anaona kuti mwalawo wagubuduzidwa kale ngakhale kuti unali waukulu kwambiri.+ Luka 24:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma anapeza kuti mwala wagubuduzidwa pamanda achikumbutsowo,+
4 Koma atayang’anitsitsa, anaona kuti mwalawo wagubuduzidwa kale ngakhale kuti unali waukulu kwambiri.+