Maliko 16:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Inuyo pitani, mukauze ophunzira ake komanso Petulo kuti, ‘Watsogola kupita ku Galileya.+ Kumeneko mukamuona, monga anakuuzirani.’”+
7 Inuyo pitani, mukauze ophunzira ake komanso Petulo kuti, ‘Watsogola kupita ku Galileya.+ Kumeneko mukamuona, monga anakuuzirani.’”+