Mateyu 26:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Koma ndikadzauka kwa akufa, ndidzatsogola kukafika ku Galileya inu musanafikeko.”+ 1 Akorinto 15:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno anaonekeranso kwa abale oposa 500 pa nthawi imodzi, ndipo ambiri a iwo akali ndi moyo mpaka lero,+ koma ena anagona mu imfa.
6 Ndiyeno anaonekeranso kwa abale oposa 500 pa nthawi imodzi, ndipo ambiri a iwo akali ndi moyo mpaka lero,+ koma ena anagona mu imfa.