Mateyu 14:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Nthawi yomweyo Yesu anatambasula dzanja lake ndi kum’gwira dzanja n’kumuuza kuti: “Wachikhulupiriro chochepa iwe, n’chifukwa chiyani wakayikira?”+
31 Nthawi yomweyo Yesu anatambasula dzanja lake ndi kum’gwira dzanja n’kumuuza kuti: “Wachikhulupiriro chochepa iwe, n’chifukwa chiyani wakayikira?”+