Salimo 83:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kuti anthu adziwe+ kuti inu, amene dzina lanu ndinu Yehova,+Inu nokha ndinu Wam’mwambamwamba,+ wolamulira dziko lonse lapansi.+ Yesaya 64:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Komatu inu Yehova, inu ndinu Atate wathu.+ Ife ndife dongo+ ndipo inu ndinu Wotiumba.+ Tonsefe ndife ntchito ya manja anu.+
18 Kuti anthu adziwe+ kuti inu, amene dzina lanu ndinu Yehova,+Inu nokha ndinu Wam’mwambamwamba,+ wolamulira dziko lonse lapansi.+
8 Komatu inu Yehova, inu ndinu Atate wathu.+ Ife ndife dongo+ ndipo inu ndinu Wotiumba.+ Tonsefe ndife ntchito ya manja anu.+