Maliko 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsopano Yohane ataponyedwa m’ndende, Yesu anapita ku Galileya+ kukalalikira uthenga wabwino wa Mulungu+ Maliko 1:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Iye anapitadi ndipo anali kulalikira m’masunagoge mwawo mu Galileya yense ndi kutulutsa ziwanda.+
14 Tsopano Yohane ataponyedwa m’ndende, Yesu anapita ku Galileya+ kukalalikira uthenga wabwino wa Mulungu+