-
Maliko 6:55Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
55 Choncho anthu am’dera lonselo anathamanga uku ndi uku ndi kunyamula odwala onse pamachira, kupita nawo kumene anamva kuti iye ali kumeneko.
-