Mateyu 18:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 ndi kunena kuti: “Ndithu ndikukuuzani, Mukapanda kutembenuka n’kukhala ngati ana aang’ono,+ simudzalowa mu ufumu wakumwamba.+ Yohane 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yesu anayankha kuti: “Ndithudi ndikukuuza, Munthu sangathe kulowa mu ufumu wa Mulungu atapanda kubadwa mwa madzi+ ndi mzimu.+
3 ndi kunena kuti: “Ndithu ndikukuuzani, Mukapanda kutembenuka n’kukhala ngati ana aang’ono,+ simudzalowa mu ufumu wakumwamba.+
5 Yesu anayankha kuti: “Ndithudi ndikukuuza, Munthu sangathe kulowa mu ufumu wa Mulungu atapanda kubadwa mwa madzi+ ndi mzimu.+