Mateyu 18:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Pamenepo mbuye wakeyo anakwiya,+ ndipo anamupereka kwa oyang’anira ndende, mpaka pamene adzabweze ngongole yonse. Luka 12:59 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 59 Ndithu ndikukuuza, Sudzatulukamo kufikira utapereka kakhobidi kotsiriza kochepa mphamvu kwambiri.”+
34 Pamenepo mbuye wakeyo anakwiya,+ ndipo anamupereka kwa oyang’anira ndende, mpaka pamene adzabweze ngongole yonse.
59 Ndithu ndikukuuza, Sudzatulukamo kufikira utapereka kakhobidi kotsiriza kochepa mphamvu kwambiri.”+