Yesaya 66:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 66 Yehova wanena kuti: “Kumwamba ndiko mpando wanga wachifumu,+ ndipo dziko lapansi ndilo chopondapo mapazi anga.+ Kodi anthu inu mungandimangire nyumba yotani?+ Ndipo malo oti ine ndingapumulirepo, ali kuti?”+ Maliro 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Chifukwa chokwiya, Yehova waphimba mwana wamkazi wa Ziyoni ndi mtambo+ wakuda.Iye waponya pansi chokongoletsera+ Isiraeli kuchokera kumwamba.+Sanakumbukire chopondapo mapazi+ ake pa tsiku la mkwiyo wake.
66 Yehova wanena kuti: “Kumwamba ndiko mpando wanga wachifumu,+ ndipo dziko lapansi ndilo chopondapo mapazi anga.+ Kodi anthu inu mungandimangire nyumba yotani?+ Ndipo malo oti ine ndingapumulirepo, ali kuti?”+
2 Chifukwa chokwiya, Yehova waphimba mwana wamkazi wa Ziyoni ndi mtambo+ wakuda.Iye waponya pansi chokongoletsera+ Isiraeli kuchokera kumwamba.+Sanakumbukire chopondapo mapazi+ ake pa tsiku la mkwiyo wake.