Luka 11:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho ngati inu, ngakhale kuti ndinu oipa, mumadziwa kupatsa ana anu+ mphatso zabwino, kuli bwanji Atate wakumwamba! Ndithudi iye adzapereka mowolowa manja mzimu woyera+ kwa amene akum’pempha.”
13 Choncho ngati inu, ngakhale kuti ndinu oipa, mumadziwa kupatsa ana anu+ mphatso zabwino, kuli bwanji Atate wakumwamba! Ndithudi iye adzapereka mowolowa manja mzimu woyera+ kwa amene akum’pempha.”