Luka 6:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Koma amene akumva ndi kusachita,+ ali ngati munthu womanga nyumba yopanda maziko padothi. Apanso mtsinje unasefukira n’kuwomba nyumbayo, ndipo nthawi yomweyo inagwa, mwakuti kugwa+ kwa nyumba imeneyo kunali kwamkokomo.”+ Yakobo 1:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pakuti ngati munthu ali wongomva mawu, koma wosachita,+ ali ngati munthu wodziyang’anira nkhope yake pagalasi.
49 Koma amene akumva ndi kusachita,+ ali ngati munthu womanga nyumba yopanda maziko padothi. Apanso mtsinje unasefukira n’kuwomba nyumbayo, ndipo nthawi yomweyo inagwa, mwakuti kugwa+ kwa nyumba imeneyo kunali kwamkokomo.”+
23 Pakuti ngati munthu ali wongomva mawu, koma wosachita,+ ali ngati munthu wodziyang’anira nkhope yake pagalasi.