Maliko 1:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Pamenepo anagwidwa chifundo,+ ndipo anatambasula dzanja lake n’kumukhudza. Kenako anamuuza kuti: “Ndikufuna. Khala woyera.”+
41 Pamenepo anagwidwa chifundo,+ ndipo anatambasula dzanja lake n’kumukhudza. Kenako anamuuza kuti: “Ndikufuna. Khala woyera.”+