Mateyu 25:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ponyani kapolo wopanda pake ameneyu kunja kumdima. Kumeneko kudzakhala kulira ndi kukukuta mano.’+
30 Ponyani kapolo wopanda pake ameneyu kunja kumdima. Kumeneko kudzakhala kulira ndi kukukuta mano.’+