Luka 5:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Zimenezi zitachitika iye anachokako. Kenako anaona wokhometsa msonkho wotchedwa Levi atakhala pansi mu ofesi yokhomera msonkho. Ndipo anamuuza kuti: “Ukhale wotsatira wanga.”+ Luka 5:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Pamenepo Leviyo anasiya chilichonse,+ ndipo ananyamuka n’kumutsatira.
27 Zimenezi zitachitika iye anachokako. Kenako anaona wokhometsa msonkho wotchedwa Levi atakhala pansi mu ofesi yokhomera msonkho. Ndipo anamuuza kuti: “Ukhale wotsatira wanga.”+