Luka 12:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho zimene mumanena mumdima zidzamveka poyera, zimene mumanong’ona kwanokha m’zipinda zanu zidzalalikidwa pamadenga.+
3 Choncho zimene mumanena mumdima zidzamveka poyera, zimene mumanong’ona kwanokha m’zipinda zanu zidzalalikidwa pamadenga.+