Yohane 5:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 ndipo adzatuluka. Amene anali kuchita zabwino adzauka kuti alandire moyo.+ Amene anali kuchita zoipa adzauka kuti aweruzidwe.+ Chivumbulutso 20:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Nyanja inapereka akufa amene anali mmenemo. Nayonso imfa ndi Manda zinapereka akufa+ amene anali mmenemo. Aliyense wa iwo anaweruzidwa malinga ndi ntchito zake.+
29 ndipo adzatuluka. Amene anali kuchita zabwino adzauka kuti alandire moyo.+ Amene anali kuchita zoipa adzauka kuti aweruzidwe.+
13 Nyanja inapereka akufa amene anali mmenemo. Nayonso imfa ndi Manda zinapereka akufa+ amene anali mmenemo. Aliyense wa iwo anaweruzidwa malinga ndi ntchito zake.+