Ekisodo 29:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Adye zinthu zimene aphimbira machimo kuti apatsidwe mphamvu ndi kuyeretsedwa.+ Koma munthu wamba asadye nawo, chifukwa ndi zinthu zopatulika.+ Luka 6:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kodi simunawerenge kuti analowa m’nyumba ya Mulungu ndi kutenga mitanda ya mkate woonetsa kwa Mulungu+ n’kudya, ndipo ina anapatsa amuna amene anali naye limodzi? Malamulo salola aliyense kudya mkate umenewu koma ansembe okha.”+
33 Adye zinthu zimene aphimbira machimo kuti apatsidwe mphamvu ndi kuyeretsedwa.+ Koma munthu wamba asadye nawo, chifukwa ndi zinthu zopatulika.+
4 Kodi simunawerenge kuti analowa m’nyumba ya Mulungu ndi kutenga mitanda ya mkate woonetsa kwa Mulungu+ n’kudya, ndipo ina anapatsa amuna amene anali naye limodzi? Malamulo salola aliyense kudya mkate umenewu koma ansembe okha.”+