Luka 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Atamwaza maso uku ndi uku kuwayang’ana onsewo, anauza munthu uja kuti: “Tambasula dzanja lako.” Munthuyo anachitadi zimenezo, ndipo dzanja lakelo linakhalanso labwinobwino.+
10 Atamwaza maso uku ndi uku kuwayang’ana onsewo, anauza munthu uja kuti: “Tambasula dzanja lako.” Munthuyo anachitadi zimenezo, ndipo dzanja lakelo linakhalanso labwinobwino.+