Yohane 7:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Komabe ochuluka m’khamu la anthulo anakhulupirira mwa iye+ ndipo anayamba kunena kuti: “Akadzafika Khristu, kodi adzachita zizindikiro zochuluka+ kuposa zimene munthu uyu wachita?”
31 Komabe ochuluka m’khamu la anthulo anakhulupirira mwa iye+ ndipo anayamba kunena kuti: “Akadzafika Khristu, kodi adzachita zizindikiro zochuluka+ kuposa zimene munthu uyu wachita?”