Luka 11:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Monga momwe Yona+ anakhalira chizindikiro kwa anthu a ku Nineve, Mwana wa munthu adzakhalanso chizindikiro ku m’badwo uwu.
30 Monga momwe Yona+ anakhalira chizindikiro kwa anthu a ku Nineve, Mwana wa munthu adzakhalanso chizindikiro ku m’badwo uwu.