Maliko 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mbewu zina zinagwera pamiyala pamene panalibe dothi lokwanira, ndipo zinamera mwamsanga chifukwa dothilo linali losazama.+ Luka 8:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Zina zinagwera pathanthwe. Koma zitamera, zinauma chifukwa panalibe chinyontho.+
5 Mbewu zina zinagwera pamiyala pamene panalibe dothi lokwanira, ndipo zinamera mwamsanga chifukwa dothilo linali losazama.+