Salimo 37:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Woipa akukonzera chiwembu munthu wolungama,+Ndipo akumukukutira mano.+ Miyambo 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakamwa pa wolungama m’pamene pamachokera moyo,+ koma pakamwa pa anthu oipa pamabisa zachiwawa.+